Thu Apr 18 2024 12:00:20 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 12:00:22 +02:00
parent 96c0b1d51c
commit 60462de10b
4 changed files with 3 additions and 1 deletions

1
16/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 16 \v 1 Mchaka cha 36 cha ulamuliro wa Asa, Basa mfumu ya Isiraeli anaukira Yuda ndipo anamanga mzinda wa Rama, kuti asalole aliyense kutuluka kapena kulowa mdziko la Asa mfumu ya Yuda.

1
16/02.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 2 Pamenepo Asa anatulutsa siliva ndi golide mzosungiramo za mnyumba ya Yehova, ndi za mnyumba ya mfumu, nazitumiza kwa Beni-hadadi mfumu ya Aramu, wakukhala ku Damasiko. Iye anati: \v 3 “Pakhale pangano pakati pa ine ndi iwe, monga linali pakati pa bambo anga ndi atate wako. Taonani, ndakutumizirani siliva ndi golide. ine ndekha."

1
16/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 \v 5 Beni-hadadi anamvera Mfumu Asa ndipo anatumiza akuluakulu a asilikali ake kukamenyana ndi mizinda ya Isiraeli. Anakantha Ijoni, Dani, Abele Maimu , ndi midzi yonse yosungiramo zinthu ya Nafitali. Ndiyeno Basa atamva zimenezi, anasiya kumanga mzinda wa Rama nkuimitsa ntchito yake. \v 6 Kenako mfumu Asa anatenga Ayuda onse pamodzi naye. Anatenga miyala ndi matabwa a ku Rama, zimene Basa ankamangira mzindawo. Kenako Mfumu Asa anagwiritsa ntchito zomangirazo pomanga Geba ndi Mizipa.

View File

@ -175,7 +175,6 @@
"16-title",
"16-01",
"16-02",
"16-04",
"16-07",
"16-09",
"16-11",