Thu Apr 18 2024 11:24:16 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 11:24:16 +02:00
parent 746e40faec
commit 5f42c518d7
4 changed files with 3 additions and 1 deletions

1
12/02.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 2 Mchaka chachisanu cha Mfumu Rehobowamu, + Sisaki mfumu ya Iguputo inabwera kudzamenyana ndi Yerusalemu chifukwa anthuwo sanalakwire Yehova. \v 3 Anadza ndi magareta mazana khumi ndi awiri, ndi apakavalo zikwi makumi asanu ndi limodzi. Ankhondo osawerengeka anadza naye ku Igupto: Alibiya, Suki, ndi Akusi. \v 4 Analanda mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri ya Yuda nkupita ku Yerusalemu.

1
12/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Tsopano mneneri Semaya anabwera kwa Rehobowamu ndi kwa atsogoleri a Yuda amene anasonkhana ku Yerusalemu chifukwa cha Sisaki. Semaya anati kwa iwo, Atero Yehova, Inu mwandisiya ine, chotero inenso ndakuperekani mdzanja la Sisaki. \v 6 Pamenepo akalonga a Israyeli ndi mfumu anadzichepetsa, nati, Yehova ndiye wolungama.

1
12/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Yehova ataona kuti adzicepetsa, mau a Yehova anadza kwa Semaya, kuti, Adzicepetsa, sindidzawaononga; Ngakhale zili choncho, adzakhala atumiki ake, kuti amvetse tanthauzo la kunditumikira + ndi kutumikira olamulira a mayiko ena.”

View File

@ -140,7 +140,6 @@
"12-01",
"12-02",
"12-05",
"12-07",
"12-09",
"12-11",
"12-13",