Thu Dec 09 2021 17:18:42 GMT-0700 (Mexican Pacific Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-12-09 17:18:42 -07:00
parent 9a01bda492
commit 493b59e7a6
3 changed files with 3 additions and 3 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 19 Mikango khumi ndi iwiri inkaimirira pamakwereropo, wina mbali iyi ndi imodzi ya masitepe asanu ndi limodziwo. Panalibe mpando wachifumu wofanana nawo muufumu wina uliwonse. \v 20 Zikho zonse zomweramo Mfumu Solomo zinali zagolide, ndipo zikho zonse zakumwa mu Nyumba ya Nkhalango ya Lebanoni zinali za golide woyenga bwino. Siliva sankaonedwa ngati ofunika m'masiku a Solomo. \v 21 Mfumuyo inali ndi zombo zapanyanja zambiri, pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pakatha zaka zitatu zombozi zimabweretsa golide, siliva, minyanga ya njovu, komanso anyani ndi anyani.
\v 19 Mikango khumi ndi zibili zinaimilila pamakwelelo, wina mbali iyi ndi imodzi ya masitepe asanu ndi limodziwo. Panalibe mpando wachifumu wofanana nawo muufumu wina uliwonse. \v 20 Zikho zonse zomweramo Mfumu Solomo zinali zagolide, ndipo zikho zonse zakumwa mu Nyumba ya Nkhalango ya Lebanoni zinali za golide woyenga bwino. Siliva sankaonedwa ngati ofunika m'masiku a Solomo. \v 21 Mfumuyo inali ndi zombo zapanyanja zambiri, pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pakatha zaka zitatu zombozi zimabweretsa golide, siliva, minyanga ya njovu, komanso anyani ndi anyani.

View File

@ -1 +1 @@
\v 22 Momwemo Mfumu Solomoni inachila mafumu yonse ya maziko yapansi mu chuma ndi nzelu. \v 23 Mafumu yonse yapa ziko lapansi yamafuna pamenso pa Solomoni kuti banvele nzelu zake, zamene Mulungu anaziyika mumutima mwake. \v 24 Bamabwela kuzapeleka musonko, zibiya zasiliva ndi zagolide, zovala, zida zankhondo, ndi zonunkhiritsa, komanso akavalo n nyulu, chaka ndi chaka.
\v 22 Momwemo Mfumu Solomoni inachila mafumu yonse ya maziko yapansi mu chuma ndi nzelu. \v 23 Mafumu yonse yapa ziko lapansi yamafuna pamenso pa Solomoni kuti banvele nzelu zake, zamene Mulungu anaziyika mumutima mwake. \v 24 Bamabwela kuzapeleka musonko, zibiya zasiliva ndi zagolide, zovala, zida zankhondo, ndi zonunkhiritsa, komanso akavalo na nyulu, chaka na chaka.

View File

@ -130,7 +130,7 @@
"09-13",
"09-15",
"09-17",
"09-19",
"09-22",
"09-25",
"09-27",
"09-29",