Mon Dec 13 2021 16:50:27 GMT+0000 (Greenwich Mean Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-12-13 16:50:27 +00:00
parent 864fba5b13
commit 4527330533
3 changed files with 3 additions and 3 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\c 23 \v 1 Muchaka cha 7, Yehoida anaonesa mphamvu zake na kuchita chipangano naba sogoleli ba magulu ya bantu muma gulu 100, Azariya mwana wa Yerohamu, Ismayeli mwana wa Yehohanani, Azariya mwana wa Obedi, Maseya mwana wa Adaya, na Elisafati mwana wa Zikiri. \v 2 Banayendayenda mu Yuda na kusonkana Alevi kuchokela mumizinda zonse za Yuda, na basogoleli ba mabanja ya Israyeli, ndipo banabwela ku Yerusalemu. \v 3 Zonse msonkano zina panga pangano na mfumu munyumba ya Mulungu; Yehoyada anababuza kuti, “Onani, mwana wa mfumu azalamulila monga mwamene Yehova anakambila pali zokuza bazikulu ba Davide.
\c 23 \v 1 Muchaka cha 7, Yehoida anaonesa mphamvu zake na kuchita chipangano naba sogoleli ba magulu ya bantu muma gulu 100, Azariya mwana wa Yerohamu, Ismayeli mwana wa Yehohanani, Azariya mwana wa Obedi, Maseya mwana wa Adaya, na Elisafati mwana wa Zikiri. \v 2 Banayendayenda mu Yuda na kusonkana Alevi kuchokela mumizinda zonse za Yuda, na basogoleli ba mabanja ya Israyeli, ndipo banabwela ku Yerusalemu. \v 3 Zonse msonkano zina panga pangano na mfumu munyumba ya Mulungu; Yehoyada anababuza kuti, “Onani, mwana wa mfumu azalamulila monga mwamene Yehova anakambila pali bana naba bazikulu ba Davide.

View File

@ -1 +1 @@
\v 4 Ichi nde chamene mufunikila kuchita: Gawo imozi wa magawo yatatu ya nsembe na Alevi bamene wamabwela kuzatumikila pa Sabata bazankala balonda pakhomo. \v 5 Winangu wachitatu azankala kunyumba ya mfumu, ndipo winangu wachitatu azankala pachipata. Bantu bonse bazankala palubanza ya nyumba ya Yehova.
\v 4 Ichi ndiye chamene mufunikila kuchita: Gawo imozi wa magawo yatatu ya nsembe na Alevi bamene wamabwela kuzatumikila pa Sabata bazankala balonda pakhomo. \v 5 Winangu wachitatu azankala kunyumba ya mfumu, ndipo winangu wachitatu azankala pachipata. Bantu bonse bazankala palubanza ya nyumba ya Yehova.

View File

@ -267,7 +267,7 @@
"22-09",
"22-10",
"23-title",
"23-04",
"23-01",
"23-06",
"23-08",
"23-10",