Thu Dec 09 2021 12:17:24 GMT+0000 (Greenwich Mean Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-12-09 12:17:24 +00:00
parent 9d2284f3b7
commit 3ba11df4c7
3 changed files with 3 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 8 Mwaicho mfumu inalamula, banatenga likasa, nakuika panja pakomo pa nyumba ya Yehova. \v 9 Mwaicho analengiza pakati pa Yuda na Yerusalemu, kuti bantu abelese kwa Yehova musonko wamene Mose mtumiki wa Mulungu aalipila Israeli muchipululu. \v 10 Asogoleli bonse na bantu bonse banakondwela na ikubwelesa ndalama ndikuziyika m'bokosi mpaka atamaliza kudzaza.
\v 8 Mwaicho mfumu inalamula, banatenga likasa, nakuika panja pakomo pa nyumba ya Yehova. \v 9 Mwaicho analengiza pakati pa Yuda na Yerusalemu, kuti bantu abelese kwa Yehova musonko wamene Mose mtumiki wa Mulungu aalipila Israeli muchipululu. \v 10 Asogoleli bonse na bantu bonse banakondwela na kubwelesa ndalama na kuziyika mubokosi mpaka bana siliza kufakamo.

View File

@ -1 +1 @@
\v 11 Nthawi zonse akaponya bokosilo kwa akalonga a mfumu ndi dzanja la Alevi, ndipo akangoona kuti muli ndalama zambiri, mlembi wa mfumu ndi wantchito wa mkulu wa ansembe ankabwera, kukachotsa bokosilo, nalitenga, mubwerere naye kumalo ake. Ankachita izi tsiku ndi tsiku, akusonkhanitsa ndalama zambiri. \v 12 Mfumu ndi Yehoyada anapereka ndalamazo kwa iwo amene anali kugwira ntchito yotumikira m'nyumba ya Yehova. Anthuwa analemba ganyu amisiri amiyala ndi amisiri a matabwa kuti akonzenso nyumba ya Yehova, ndiponso ogwira ntchito zachitsulo ndi zamkuwa.
\v 11 Ntawi yonse akaponya bokosilo kwa akalonga a mfumu ndi dzanja la Alevi, ndipo akangoona kuti muli ndalama zambiri, mlembi wa mfumu ndi wantchito wa mkulu wa ansembe ankabwera, kukachotsa bokosilo, nalitenga, mubwerere naye kumalo ake. Ankachita izi tsiku ndi tsiku, akusonkhanitsa ndalama zambiri. \v 12 Mfumu ndi Yehoyada anapereka ndalamazo kwa iwo amene anali kugwira ntchito yotumikira m'nyumba ya Yehova. Anthuwa analemba ganyu amisiri amiyala ndi amisiri a matabwa kuti akonzenso nyumba ya Yehova, ndiponso ogwira ntchito zachitsulo ndi zamkuwa.

View File

@ -281,6 +281,7 @@
"24-01",
"24-04",
"24-06",
"24-08",
"24-13",
"24-15",
"24-17",