Thu Apr 18 2024 11:16:13 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 11:16:14 +02:00
parent 65170d9384
commit 2d4db9c00b
4 changed files with 3 additions and 1 deletions

1
11/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Ansembe ndi Alevi amene anali mu Isiraeli yense anapita kwa iye kuchokera mmalire awo. \v 14 Pakuti Alevi anasiya malo awo odyetserako ziweto ndi chuma chawo kuti abwere ku Yuda ndi ku Yerusalemu, pakuti Yerobiamu ndi ana ake anawathamangitsa, moti sanathenso kukhala ansembe a Yehova. \v 15 Yerobiamu anadzipangira ansembe a malo okwezeka, ndi mbuzi ndi ana a ng'ombe amene anapanga.

1
11/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Anthu a mmafuko onse a Isiraeli anatsatira pambuyo pawo, amene anali kufunitsitsa kufunafuna Yehova Mulungu wa Isiraeli. anafika ku Yerusalemu kudzapereka nsembe kwa Yehova Mulungu wa makolo awo. \v 17 Chotero analimbitsa ufumu wa Yuda ndi kulimbitsa Rehobowamu mwana wa Solomo mzaka zitatu, ndipo anayenda mnjira ya Davide ndi Solomo zaka zitatu.

1
11/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 \v 19 Rehobowamu anadzitengera mkazi: Mahalati, mwana wamkazi wa Yerimoti, mwana wa Davide, ndi Abihaili, mwana wamkazi wa Eliyabu, mwana wa Jese. Iye anamuberekera ana aamuna: Yeusi, Semariya ndi Zahamu.

View File

@ -133,7 +133,6 @@
"11-11",
"11-13",
"11-16",
"11-18",
"11-20",
"11-22",
"12-title",