From 0f265421c5a4aa4d6626d7def801b99639781be0 Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: Muzgatama Date: Thu, 18 Apr 2024 12:10:01 +0200 Subject: [PATCH] Thu Apr 18 2024 12:10:00 GMT+0200 (South Africa Standard Time) --- 17/07.txt | 2 +- 17/10.txt | 1 + 17/12.txt | 1 + manifest.json | 1 + 4 files changed, 4 insertions(+), 1 deletion(-) create mode 100644 17/10.txt create mode 100644 17/12.txt diff --git a/17/07.txt b/17/07.txt index ab238e1..997c4c7 100644 --- a/17/07.txt +++ b/17/07.txt @@ -1 +1 @@ -\v 7 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wake, anatumiza akalonga ake, Beni-Haili, Obadiya, Zekariya, Netaneli ndi Mikaya kuti akaphunzitse m’mizinda ya Yuda. \v 8 pamodzi ndi Alevi: Semaya, Netaniya, Zebadiya, Asaheli, Semiramoti, Yehonatani, Adoniya, Tobiya, ndi Tobi-Adoniya; ndi pamodzi nao panali Elisama ndi Yehoramu ansembe. \v 9 Anaphunzitsa m’Yuda, ali nalo buku la chilamulo cha Yehova; Iwo anayendayenda m’mizinda yonse ya Yuda ndi kuphunzitsa pakati pa anthu. \ No newline at end of file +\v 7 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wake, anatumiza akalonga ake, Beni-Haili, Obadiya, Zekariya, Netaneli ndi Mikaya kuti akaphunzitse m’mizinda ya Yuda. \v 8 Pamodzi ndi Alevi: Semaya, Netaniya, Zebadiya, Asaheli, Semiramoti, Yehonatani, Adoniya, Tobiya, ndi Tobi-Adoniya; ndi pamodzi nao panali Elisama ndi Yehoramu ansembe. \v 9 Anaphunzitsa m’Yuda, ali nalo buku la chilamulo cha Yehova; Iwo anayendayenda m’mizinda yonse ya Yuda ndi kuphunzitsa pakati pa anthu. \ No newline at end of file diff --git a/17/10.txt b/17/10.txt new file mode 100644 index 0000000..0ec1249 --- /dev/null +++ b/17/10.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 10 Mantha a Yehova anagwera maufumu onse a maiko ozungulira Yuda, kotero kuti sanachite nkhondo ndi Yehosafati. \v 11 Afilisti ena anapatsa Yehosafati mphatso, ndi siliva ngati msonkho. Aarabu anam’bweretseranso nkhosa, nkhosa 7,700, ndi mbuzi 7,700. \ No newline at end of file diff --git a/17/12.txt b/17/12.txt new file mode 100644 index 0000000..2b1f85b --- /dev/null +++ b/17/12.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 12 Yehosafati anakhala wamphamvu kwambiri. Anamanga mipanda yolimba kwambiri ndi mizinda yosungirako zinthu m’Yuda. \v 13 Anali ndi katundu wambiri m’mizinda ya Yuda, ndi asilikali—ankhondo amphamvu—m’Yerusalemu. \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index 09cdb6f..1ba12b5 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -184,6 +184,7 @@ "17-01", "17-03", "17-05", + "17-07", "17-10", "17-12", "17-14",