Tue Dec 24 2019 11:41:33 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-12-24 11:41:34 +02:00
parent 6fbdbec964
commit 76fd150cb0
7 changed files with 12 additions and 6 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 4 Zoonadi, pamene tinali na inu, tinakuuzani poyamba kuti tinali kufunika kubvutika, ndipo izi zinachitika, monga muziba. \v 5 mwa ichi, pamene sininakwanise kuimilira, ninatuma kuti nizibe za chikulupiliro chanu. mwina oyesa uja anakuyesani mu njira ina yake, na nchito yathu inali yopanda phindu.
\v 4 Zoonadi, pamene tinali na inu, tinakuuzani poyamba kuti tinali kufunika kubvutika, ndipo izi zinachitika, monga muziba. \v 5 Mwa ichi, pamene sininakwanise kuimilira, ninatuma kuti nizibe za chikulupiliro chanu. mwina oyesa uja anakuyesani mu njira ina yake, na nchito yathu inali yopanda phindu.

View File

@ -1 +1 @@
\v 6 \v 7 koma timoteyo anabwera kuchoka kwa inu na kuleta kwa ise uthenga wabwino wa chikulupiliro na chikondi. anatiuza kuti mumatikumbukira, na kuti mufuna kutionanso monga mwamene ise tifunila kukuonani. chifukwa cha ichi, abale, tinatonthozedwa chifukwa cha chikulupiliro chanu, mumabvuto yathu yonse na kunzunzidwa.
\v 6 Koma timoteyo anabwera kuchoka kwa inu na kuleta kwa ise uthenga wabwino wa chikulupiliro na chikondi. anatiuza kuti mumatikumbukira, na kuti mufuna kutionanso monga mwamene ise tifunila kukuonani. \v 7 chifukwa cha ichi, abale, tinatonthozedwa chifukwa cha chikulupiliro chanu, mumabvuto yathu yonse na kunzunzidwa.

View File

@ -1 +1 @@
\v 8 \v 9 \v 10 tsopano tili na moyo, ngati muimilira mwa ambuye. nimatokozo ya bwanji yamene tingapase mulungu pa inu, pa chimwemwe chonse chamene tili nacho pamenso pa mulungu cha inu? usiku na muzuba timakupemphelerani na mphamvu kuti tione nkhope yanu na kukupasani chamene chipelebera pa chikulupiliro chanu.
\v 8 tsopano tili na moyo, ngati muimilira mwa ambuye. \v 9 nimatokozo ya bwanji yamene tingapase mulungu pa inu, pa chimwemwe chonse chamene tili nacho pamenso pa mulungu cha inu? \v 10 usiku na muzuba timakupemphelerani na mphamvu kuti tione nkhope yanu na kukupasani chamene chipelebera pa chikulupiliro chanu.

View File

@ -1 +1 @@
\v 11 \v 12 \v 13 lekani mulungu atate athu yeve, na ambuye yesu, atipase njira yofika kwa inu. mulungu akupangiseni kuti mukule mu chikondi cha wina na mnzake na banthu bonse, mwamene naise tichitira kwa inu. alimbise mitima yanu, kuti yankhale yopanda zodesa mu chiyelo pa menso pa mulungu atate, pa kubwera kwa ambuye yesu na bonse boyera.
\v 11 lekani mulungu atate athu yeve, na ambuye yesu, atipase njira yofika kwa inu. \v 12 mulungu akupangiseni kuti mukule mu chikondi cha wina na mnzake na banthu bonse, mwamene naise tichitira kwa inu. \v 13 alimbise mitima yanu, kuti yankhale yopanda zodesa mu chiyelo pa menso pa mulungu atate, pa kubwera kwa ambuye yesu na bonse boyera.

1
04/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 4 Mosi

View File

@ -1 +1 @@
mutu 4
Mutu 4

View File

@ -54,6 +54,11 @@
"02-14",
"02-17",
"03-title",
"03-01"
"03-01",
"03-04",
"03-06",
"03-08",
"03-11",
"04-title"
]
}