nya-x-nyanja_1ki_text_reg/20/35.txt

1 line
351 B
Plaintext

\v 35 Muntu winango, umozi pali bana ba baneneli, anakamba kuli munzake kupitila mu mau ya Yehova, "Napapata nimenye." Koma mwamuna anakana kumumenya. \v 36 Mwaicho muneneli anakamba kuli muneneli munzake, "Chifukwa sunamvele mawu ya Yehova, pamene apo ukanisiya, nkalamu izakupaya." Pamene apo mwamuna anayenda, nkalamu inabwela pali eve na kumupaya.