nya-x-nyanja_1ki_text_reg/20/31.txt

1 line
515 B
Plaintext

\v 31 Bancito ba Ben Hadadi banakamba kuli eve, "Ona manje, tamvela kuti mfumu za nyumba ya Isirayeli ni mfumu zachifundo.Napapata tiyeni timange vovala vamasaka muchiuno mwatu na ntambo kumitu zatu, na kuyenda kuli mfumu yaku Isirayeli.Mwamwai azapulumusa umoyo wako. " \v 32 Mwaicho banavala vovala vamasaka muchiuno na ntambo mumitu zao na kuyenda kuli mfumu ya Isirayeli nakukamba ati, "wanchito wanu Ben Hadadi anakamba, 'Napapata lekani ninkale wa moyo.'” Ahabu anakamba, "akali wa moyo? ni mubale wanga. "