nya-x-nyanja_1ki_text_reg/20/28.txt

1 line
282 B
Plaintext

\v 28 Pamene apo muntu wa Mulungu anabwela pafupi na kukamba na mfumu ya Isirayeli ati, " Yehova akamba: 'Chifukwa ba Aaramu bakamba kuti Yehova ndiye mulungu wa kumapili, koma si Mulungu wa vigwa, nizaika iyi gulu yambili ya nkondo mukwanja yako ndipo uzaziba kuti ndine Yehova.""