nya-x-nyanja_1ki_text_reg/20/11.txt

1 line
399 B
Plaintext

\v 11 Mfumu ya Israeli inayanka nakukamba ati, "Uza Beni-Hadadi kuti, 'Palibe wamene avala zida zake ayenela kuzimvela monga azaivula.'” \v 12 Ben Hadadi anamvela utenga uwu pamene anali kumwa, eve na mfumu zinali pansi pake zamene zinali mumahema zawo. Ben Hadadi analamula banchito bake kuti, "Konzekelani nkondo." pamene apo banakonzekela mumalo ya nkondo kuti bamenyane na muzinda na muzinda.