nya-x-nyanja_1ki_text_reg/20/09.txt

1 line
455 B
Plaintext

\v 9 Pamenepo Ahabu anauza bautenga ba Beni-hadadi kuti, "Uzani mbuye wanga mfumu kuti, 'Nivomeleza pavonse kuti munatumiza kapolo wanu kuchita paulendo woyamba, koma sinizavomela futi .'” ndipo ntumi zinachoka nakupeleka yanko kuli Ben Hadadi. \v 10 Ndipo Ben Hadadi anatumiza yanko yake kuli Ahabu, nakukamba ati, "Milungu zinichite so chabe nakuchilapo, " ngati milota ya mu samalia ingakwanile bantu bonse bamene banikonka kutengako che mukwanja,"