nya-x-nyanja_1ki_text_reg/20/07.txt

1 line
346 B
Plaintext

\v 7 Pamene apo mfumu ya Israeli inayitana bakulu bonse ba muziko ija nakukamba ati, "Napapata zibani na kuwona mwamene muntu uyu afunila mavuto. Atumiza utenga kuli ine kuti atenge bakazi banga, bana, siliva na golide, ndipo ine sininamu kanile. " \v 8 Bakulu bonse na bantu bonse bana kamba kuli Ahabu "Musamumvele kapena kuchita vamene afuna."