nya-x-nyanja_1ki_text_reg/08/62.txt

1 line
266 B
Plaintext

\v 62 Mwaichi mfumu na bonse Israeli bonse pamozi naye anapeleka nsembe kwa Yehova. \v 63 Solomo anapereka nsembe yoyamika kwa Yehova: ng'ombe zikwi makumi awili mphambu zibilii, na nkhosa 120,000. Momwemo mfumu na bana bonse ba Israyeli banapatula nyumba ya Yehova.