nya-x-nyanja_1ki_text_reg/08/51.txt

1 line
482 B
Plaintext

\v 51 Iwo ni banthu banu bamene munabasankha, bamene munawapulumutsa ku Iguputo ngati kuti mukuwotcha chitsulo. \v 52 Maso anu yakhale otsegukila pempho la ine mtumiki wanu, na zopempha za banthu banu Israyeli, kuti muwamvere iwo, pamene iwo alira kwa inu. \v 53 Pakuti munawapatula pakati pa anthu a mitundu yonse ya paziko lapansi yankhale banu, na kulandila malonjezano anu, monga umo munalongosolela na Mose mtumiki wanu, m'mene munaturutsa makolo athu m'Aigupto, Ambuye Yehova.