nya-x-nyanja_1ki_text_reg/08/37.txt

1 line
448 B
Plaintext

\v 37 Tiyelekeze kuti muziko mwanu muli njala, kapena ngati muli matenda, chimphepo kapena kachilombo, zombe kapena malasankhuli; kapena kuti ngati mudani aukila zipata za muzi muziko yao, kapena kuti pali mulili uli wonse kapena matenda; \v 38 ndipo nichani ngati mapemphelo na zopempha zichokela kwa munthu, kapena na banthu banu bonse ba Israyeli, ali bonse aziba mulili wamene uyo mumutima mwake; atambasula manja yake kuyangana ku tempele iyi.