nya-x-nyanja_1ki_text_reg/22/51.txt

1 line
463 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 51 Ahaziya mwana wa Ahabu anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya mchaka cha 17 cha Yehosafati mfumu ya Yuda, ndipo analamulira Isiraeli zaka ziwiri. \v 52 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anayenda mnjira ya bambo ake, mnjira ya mayi ake, ndi mnjira ya Yerobiamu mwana wa Nebati, imene anachimwitsa nayo Isiraeli. \v 53 Iye anatumikira Baala ndi kumlambira, moti anakwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli, monga mmene bambo ake anachitira.