nya-x-nyanja_1ki_text_reg/22/48.txt

1 line
457 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 48 Yehosafati anamanga zombo za ku Tarisi; Anayenera kupita ku Ofiri kukatenga golide, koma sanapite chifukwa zombozo zinasweka ku Ezioni Geberi. \v 49 Pamenepo Ahaziya mwana wa Ahabu anauza Yehosafati kuti: “Atumiki anga apite limodzi ndi atumiki ako mzombo. Koma Yehosafati sanalole. \v 50 Yehosafati anagona pamodzi ndi makolo ake, naikidwa pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake; Yehoramu mwana wake anakhala mfumu mmalo mwake.