nya-x-nyanja_1ki_text_reg/09/26.txt

1 line
362 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 26 Mfumu Solomo inamanga zombo zankhondo ku Ezioni Geberi, pafupi ndi Elati mmphepete mwa Nyanja Yofiira mdziko la Edomu. \v 27 Hiramu anatumiza atumiki ku zombo za Solomo, amalinyero odziwa bwino nyanja, pamodzi ndi antchito a Solomo. \v 28 Iwo anapita ku Ofiri pamodzi ndi atumiki a Solomo. Kumeneko anabweretsa matalente 420 agolide kwa Mfumu Solomo.