nya-x-nyanja_1ki_text_reg/11/05.txt

1 line
230 B
Plaintext

\v 5 \v 6 Pakuti Solomo anatsatira Asitoreti mulungu wamkazi wa Asidoni, ndi kutsatira Moleki fano lonyansa la Aamoni. Solomoni anachita choipa pamaso pa Yehova; sanatsata Yehova ndi mtima wonse monga anachitira Davide atate wake.