nya-x-nyanja_1ki_text_reg/14/29.txt

1 line
413 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa mbuku la zochitika za mmasiku a mafumu a Yuda. \v 30 Panali nkhondo yokhazikika pakati pa Rehobowamu ndi Yerobiamu. \v 31 Choncho Rehobowamu anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anaikidwa mmanda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide. Dzina la amayi ake linali Naama Mamoni. Abiya mwana wake anakhala mfumu mmalo mwake.