nya-x-nyanja_1ki_text_reg/22/41.txt

1 line
295 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 41 Kenako Yehosafati mwana wa Asa anayamba kulamulira Yuda mchaka chachinayi cha Ahabu mfumu ya Isiraeli. \v 42 Yehosafati anali wa zaka makumi atatu kudza zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi awiri mphambu zisanu. Dzina la amayi ake linali Azuba mwana wa Sili.