\v 34 Koma munthu wina anaponya uta wake mwachisawawa, nalasa mfumu ya Israyeli pakati pa mfundo za zida zake. Pamenepo Ahabu anauza woyendetsa galeta lake kuti: “Tembenuka unditulutse kunkhondo, pakuti ndavulala kwambiri.