nya-x-nyanja_1ki_text_reg/22/16.txt

1 line
256 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 16 Pamenepo mfumu inati kwa iye, Ndidzakulumbiritsa kangati kuti usandiuze zoona zokhazokha mdzina la Yehova? \v 17 Ndipo Mikaya anati, Ndinaona Aisrayeli onse atabalalika kumapiri, ngati nkhosa zopanda mbusa; ndipo Yehova anati, Amenewa alibe mbuye;