nya-x-nyanja_1ki_text_reg/22/07.txt

1 line
496 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 7 Koma Yehosafati anati, Kodi pano palibenso mneneri wina wa Yehova amene tingapemphe malangizo kwa iye? \v 8 Mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Pali munthu mmodzi amene tingapemphe malangizo kwa Yehova kuti atithandize, ndiye Mikaya mwana wa Imla, koma ndimadana naye chifukwa salosera zabwino za ine, koma zowawa. Koma Yehosafati anati, Mfumu isatero. \v 9 Kenako mfumu ya Isiraeli inaitana kapitawo wa asilikali nkumuuza kuti: “Bwera naye Mikaya mwana wa Imla nthawi yomweyo.