nya-x-nyanja_1ki_text_reg/22/05.txt

1 line
317 B
Plaintext

\v 5 Yehosafati anauza mfumu ya Isiraeli kuti: “Chonde funsani malangizo kwa Yehova kuti muyambe kuchita chiyani. \v 6 Pamenepo mfumu ya Israyeli inasonkhanitsa aneneri mazana anai, nanena nao, Ndipite kunkhondo ku Ramoti Giliyadi, kapena ndisapite? Iwo anati, "Umbani, pakuti Yehova adzaupereka m'manja mwa mfumu."