nya-x-nyanja_1ki_text_reg/22/03.txt

1 line
379 B
Plaintext

\v 3 Ndipo mfumu ya Israyeli inati kwa anyamata ace, Kodi mudziwa kuti Ramoti-giliyadi ndi wathu, koma siticita kanthu kuulanda m'dzanja la mfumu ya Aramu? \v 4 Ndipo anati kwa Yehosafati, Kodi udzapita nane kunkhondo ku Ramoti Gileadi? Yehosafati anayankha mfumu ya Isiraeli kuti, “Ine ndili ngati inu, anthu anga ali ngati anthu anu, ndipo akavalo anga ali ngati akavalo anu.