nya-x-nyanja_1ki_text_reg/21/25.txt

1 line
250 B
Plaintext

\v 25 Panalibe munthu wonga Ahabu amene anadzigulitsa kuti achite zoipa pamaso pa Yehova, amene Yezebeli mkazi wake anamuchimwitsa. \v 26 Ahabu ananyansidwa ndi mafano, monga mwa zonse anacita Aamori, amene Yehova anawacotsa pamaso pa ana a Israyeli.