nya-x-nyanja_1ki_text_reg/20/39.txt

1 line
530 B
Plaintext

\v 39 Pamene mfumu inapitilapo, muneneli analila kuli mfumu nakukamba ati, "Wantchito wako anayenda mukutenta kwa nkondo, ndipo musilikali winanangu ana imilila nakuleta muntu kuli ine na kukamba, 'onani muntu uyu. Ngati mu njila iliyonse asoba, moyo wako uzapasiwa mumalo mwa moyo wake, olo uzafunika kulipila ndalama imozi ya siliva. ' \v 40 Koma chifukwa wanchito wako enze kungo yenda yenda uku na uku, muntu anataba. " ndipo mfumu ya Israeli inamuwuza kuti, "Ichi ndiye chizankala chilango chako- iwe mwine wake wasanka."