nya-x-nyanja_1ki_text_reg/20/37.txt

1 line
228 B
Plaintext

\v 37 Kuchoka apo muneneli anapeza muntu winango nakukamba, "Napapata nimenye." ndipo mwamuna uyo anamumenya na kumupanga chilonda. \v 38 Ndipo muneneli anayenda nakuyembekeza mfumu panjila; anali anazibis na nsalu pamenso yake.