nya-x-nyanja_1ki_text_reg/20/33.txt

1 line
518 B
Plaintext

\v 33 Manje bamuna banali kumvelela chizindikilo chilichonse chochokela kuli Ahabu, pameneapo mwamusanga banamuyanka kuti, "Ehe, mubale wako Ben Hadadi ali moyo." Mwaicho Ahabu anakamba , " yenda ukamulete." \v 34 Ndipo Ben-Hadadi anakamba kuli Ahabu, , "Nikubwezelani mizinda zamene batate banga banapoka batate banu, ndipo mungazipangile pogulisila mu Damasiko, mwamene batate banga banachitila ku Samariya." Ahabu anayanka, "Nizakuleka uyende na pangano iyi." ndipo Ahabu anachita naeve pangano, nakumuleka ayende.