nya-x-nyanja_1ki_text_reg/14/25.txt

1 line
293 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 25 Ndiyeno mchaka chachisanu cha Mfumu Rehobowamu, Sisaki mfumu ya ku Iguputo inabwera kudzamenyana ndi Yerusalemu. \v 26 Iye anatenga chuma cha mnyumba ya Yehova ndi chuma cha mnyumba ya mfumu. Iye anachotsa chirichonse; anatenganso zishango zonse zagolide zimene Solomo anapanga.