nya-x-nyanja_1ki_text_reg/13/31.txt

1 line
380 B
Plaintext

\v 31 Pamene ana mushika m'manda, mneneli mukulu anakamba anakamba kuli bana bake ba muna, kuti, "Ngati nafa mukanishike m'manda mwamene kapolo wa Mulungu anashikiwa. Ikani mabonzo yanga pafupi nama bonzo yake. \v 32 Koma uthenga ana kambilila mu mau ya Yehova, kunyamukila guwa ya nsembe mu Beteli, na manyumba yonse yakumalo yokwezeka m'mizinda ya Samariya, viza chitika zoona."