nya-x-nyanja_1ki_text_reg/13/26.txt

1 line
503 B
Plaintext

\v 26 Pamene mneneli wamene anamubwealesa kuchokela ku njila ija anakamba, "Ni kapolo wa Mulungu wamene sananvele mau ya Yehova. Chifukwa ichi Yehova anamupeleka kuli nkalamu, ndipo ana mujubajuba mutungono naku mu paya, mau ya Yehova anamuchenjeza. " \v 27 Ndipo mneneli mukulu anakamba na bana bake bamuna, kukamba, "Mangililani bulu yanga," ndipo banaimangilila. \v 28 Anayenda nakapeza tupi inasala panjila, bulu na nkalamu kuimilila pafupi na tupi. Nkalamu sinadye chitumbi kapena ku gonjesa bulu.