nya-x-nyanja_1ki_text_reg/13/14.txt

1 line
563 B
Plaintext

\v 14 Mneneli mukulu pa sogolo pa kapolo wa Mulungu anamupeza ankala pansi pa mtengo ikulu; ndipo anakamba kuli eve, Ndiwe kapoo wa Mulungu anachokela ku Yuda? Eve anayanka, "Ndine." \v 15 Ndipo mneneli mukulu anakamba kuli eve, "Bwelela naine kunyumba ukadye na chakudya." \v 16 kapolo wa Mulungu anayanka kuti, "Sindingabwelele naiwe kapena kungena naiwe, kapena kudya chakudya kapena kumwa manzi pamozi naiwe pamalo yano, \v 17 chifukwa aninilamulila Yehova kuti, 'Usadye chakudya kapena kumwa manzi kwamene uko, ndipo musabwelele njila yamene munabwelela.'”