nya-x-nyanja_1ki_text_reg/13/08.txt

1 line
395 B
Plaintext

\v 8 Kapolo wa Mulungu ana kamba kuli mfumu, "nangu unipase pakati pa chuma chako, sinizayenda naiwe, kapena kudya kapena kumwa manzi pamalo pano, \v 9 chifukwa Yehova ananilamulila mu mau yake kuti, 'Usadye mukate kapena kumwa manzi, kapena kubwelela panjila yamene wabwelela.” \v 10 kapolo wa Mulungu leka njila ina ndipo sanabwelele kunyumba kwake kupitila njila yamene anapitila ku Beteli.