nya-x-nyanja_1ki_text_reg/11/09.txt

1 line
229 B
Plaintext

\v 9 Yehova anakwiyira Solomo chifukwa mtima wake unapatuka kwa iye, Mulungu wa Isiraeli, ngakhale kuti anaonekera kwa iye kawiri, \v 10 ndipo anamulamula kuti asatsatire milungu ina. Koma Solomo sanamvere zimene Yehova anamuuza.