nya-x-nyanja_1ki_text_reg/11/03.txt

1 line
312 B
Plaintext

\v 3 Solomoni anali ndi akazi mazana asanu ndi awiri, ana aakazi, ndi adzakazi mazana atatu. Akazi ake anapatutsa mtima wake. \v 4 Pakuti pamene Solomo anakalamba, akazi ake anapambutsa mtima wake atsate milungu yina; mtima wake sunadzipereka kwathunthu kwa Yehova Mulungu wake, monga mtima wa Davide atate wake.