nya-x-nyanja_1ki_text_reg/10/16.txt

1 line
351 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 16 Mfumu Solomo inapanga zishango zazikulu mazana awiri zagolide wosakaniza ndi zitsulo zina. Masekeli mazana asanu ndi limodzi a golidi analowa m'modzi. \v 17 Anapanganso zishango mazana atatu zagolide wosakaniza ndi zitsulo zina. chishango chilichonse chinali ndi mamina atatu agolidi; mfumu inawaika mnyumba ya mfumu ya Nkhalango ya Lebanoni.