nya-x-nyanja_1ki_text_reg/10/13.txt

1 line
238 B
Plaintext

\v 13 Mfumu Solomo inapatsa mfumukazi ya ku Sheba chilichonse chimene inafuna ndi chilichonse chimene inapempha, kuwonjezera pa zimene Solomo anapatsa mfumukazi ya ku Seba. Chotero iye anabwerera kudziko la kwawo pamodzi ndi antchito ake.