This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.
\v 6 Iye anauza mfumu kuti: “Zoonadi, mbiri imene ndinaimva m’dziko langa la mawu anu ndi nzeru zanu. \v 7 Sindinakhulupirire uthengawo mpaka ndinabwera kuno, ndipo tsopano maso anga aona. Sindinauzidwe theka! Mwanzeru ndi m’chuma mwaposa mbiri imene ndinaimva.