nya-x-nyanja_1ki_text_reg/10/01.txt

1 line
304 B
Plaintext

\c 10 \v 1 Mfumu yaikazi ya ku Sheba itamva za Solomo za dzina la Yehova, inadza kudzamuyesa ndi mafunso ovuta. \v 2 Iye anafika ku Yerusalemu ndi gulu lalitali kwambiri, ngamila zonyamula zonunkhira, golide wambiri, ndi miyala yamtengo wapatali. Atafika, anauza Solomo zonse zimene zinali mumtima mwake.