nya-x-nyanja_1ki_text_reg/08/64.txt

1 line
271 B
Plaintext

\v 64 Pa siku yamene iyo mfumu inapatula pakati pa bwalo pasogolo pa tempele ya Yehova; pakuti pamenepo anapeleka nsembe zopseleza, na nsembe za mbeu, na mafuta ya nsembe zoyamika; zing'onozing'ono kulandila nsembe yopseleza, nsembe yambewu, ndi mafuta a nsembe zoyamika.