nya-x-nyanja_1ki_text_reg/08/49.txt

1 line
343 B
Plaintext

\v 49 Pamenepo kuchokera kumwamba, kwamene imwe munkala, mvelani imwe pemphero yabo na chopempa chabo kupempa tandizo, ndipo muzabalungamisa. \v 50 Mukululukire banthu banu bamene banakuchimwirani, na volakwa vawo vonse vamene banakulakwirani, ndipo mubachitire chifundo pamenso pa bamene bawagwira, na kubachitira chifundo bamene banabagwira.