nya-x-nyanja_1ki_text_reg/08/44.txt

1 line
324 B
Plaintext

\v 44 Tiyelekeze kuti anthu anu apita kukamenyana na mudani, kudzera njira iliyonse yomwe mungatumize, ndipo akuganiza kuti akupemphera kwa inu, Yehova, kumzinda umene mwasankha, komanso kunyumba imene ndamangira dzina lanu. \v 45 Kenako mverani kumwambako pemphero lawo ndi pempho lawo, ndipo athandizeni pa zomwe akuchita.