nya-x-nyanja_1ki_text_reg/08/17.txt

1 line
407 B
Plaintext

\v 17 Manje chinali mumutima wa Davide tate wanga ndi mtima womangira nyumba dzina la Yehova Mulungu wa Israyeli. \v 18 Koma Yehova anati kwa atate wanga Davide, Popeza munali mumutima mwanu kuti mumange nyumba pa zina yanga, munachita bwino kuli ichi mumitima mwanu. \v 19 Koma iwe suizamanga nyumba; Mumalo mwake, mwana wako wamwamuna, wamene azakabadwa mumusana mwako, azakamanga nyumba pa zina yanga. '