nya-x-nyanja_1ki_text_reg/08/14.txt

1 line
506 B
Plaintext

\v 14 Ndipo mfumu inapindamuka na kudalisa bonse mupingo wa Isiraeli, pamene mupingo bonse wa Isiraeli unali woimilila. \v 15 Anakamba kuti, Alemekezeke Yehova Mulungu wa Israyeli, wamene anakamba na Davide tate wanga, na kukwanilisa na manja yake, kuti, \v 16 Kuyambila siku yamene ninachosa bantu banga Israyeli mu Aigupto, sininasanke muzinda kuchoka mumitundu yonse ya Israeli kuti amange nyumba, kuti zina yanga linkale pamenepo. Mwaichi, ninasankha Davide kuti alamulile banthu banga ba Israeli. '