nya-x-nyanja_1ki_text_reg/08/09.txt

1 line
391 B
Plaintext

\v 9 Munalibe kantu mulikasa koma chabe minyala ibibli yamene Mose anaikamo ku Horebe, pamene Yehova anapanga chipangano na bana ba Israyeli, pamene banachoka muziko ya Aigupto. \v 10 Panali kuti pamene bansembe banachoka mu malo yopatulika, kumbi inazula mu tempele ya Yehova. \v 11 Bansembe sibanakwanise kuimilila chifukwa cha kumbi, chifukwa ulemelelo wa Yehova unazula mu nyumba yake.