Mon Dec 06 2021 22:34:55 GMT+0000 (Greenwich Mean Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-12-06 22:34:55 +00:00
parent da949613b6
commit feec4557f1
2 changed files with 2 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 23 Kuchokela kudya na kumwa, mneneli anakwela bulu kapolo wa Mulungu, muntu wamene anabwelela naye. \v 24 Pamene kapolo wa Mulungu anayenda, nkalamu ina mukumana panjila nakumupaya, ndipo tupi yake inasala panjila. Bulu inaimilia pambali pake, ndipo nkalamu nayeve inaimilia pafupi pa tupi. \v 25 pamene bamuna bana pita naku ona tupi ina sala panjila, ndipo nkalamu inamilila pafupi na tupi, iwo anabwera ndi kukanena mu mzindawo momwe mneneri wokalambayo amakhala.
\v 23 Kuchokela kudya na kumwa, mneneli anakwela bulu kapolo wa Mulungu, muntu wamene anabwelela naye. \v 24 Pamene kapolo wa Mulungu anayenda, nkalamu ina mukumana panjila nakumupaya, ndipo tupi yake inasala panjila. Bulu inaimilia pambali pake, ndipo nkalamu nayeve inaimilia pafupi pa tupi. \v 25 pamene bamuna bana pita naku ona tupi ina sala panjila, ndipo nkalamu inamilila pafupi na tupi, banabwela naku kamba mu mzinda mwamene mneneli mukulu enzonkala.

View File

@ -266,6 +266,7 @@
"13-14",
"13-18",
"13-20",
"13-23",
"13-29",
"13-31",
"13-33",